03/09/2026
Kodi Mwamva????
Ife a 265 Energy takubweletserani Nkhani yabwino.
Tatsitsa mtengo wa panels a 325W kuchoka pa mtengo wa Mk290,000 kufika pa mtengo ongopeleka wa Mk250,000.
Fulumirani zabwinozi zisakuphonyeni.Promotionyi itha pa 10 September. #