Chau's Garage & Workshop

Chau's Garage & Workshop The motorcycle hospital

30/03/2026

Njinga yanu pulling ili poor komanso fuel consumption ili hight
Inu ngat mmisili muunikira zinthu ziti

20/11/2025

Ngati njinga yanu omaotcha ma plug pafupi pafupi, Pali njila yoti inu mukhoza kimagula plug pa chaka kamodzi

Ndikudziwa awa ogulitsa ma spares wa Adana nane koma mawa khalani pamenepo ndikuonetseni mmene tichitira

Usiku wabwino nonse

Timasewera ndi katunduyi lero
18/11/2025

Timasewera ndi katunduyi lero

01/11/2025

Motorcycle wiring,
Something I enjoy dealing with,
Posachedwa tikhale tikuphunzita zinthu zotele

31/10/2025

Pamudzi pano posachedwa tikhala tikuphunzitsana mmene umoyo wa njinga ya moto umakhalira, ngakhalenso kuyankha ena mwamafunso amene amakuzunguzani pa njinga yanu

Stay Tuned

30/10/2025

Kwacha Tsopano,
Osaiwala kuchita check oil mu njingazo

Address

Nchalo
Chikwawa
0000

Opening Hours

Monday 09:00 - 17:00
Tuesday 09:00 - 17:00
Wednesday 09:00 - 17:00
Thursday 09:00 - 17:00
Friday 09:00 - 17:00

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chau's Garage & Workshop posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share